OKHULUPILIRA ALIYENSE NDI MBONI YA UTHENGA WABWINO 

Tonse pamodzi titha kufikila anthu 1 billion ndiuthenga wabwino m’mwenzi wa 2020! 

OKHULUPILIRA ALIYENSE NDI MBONI YA UTHENGA WABWINO 

Tonse pamodzi titha kufikila anthu 1 billion ndiuthenga wabwino m’mwenzi wa 2020! 

GO 2020 Starts Now!

Pray. Pray for 5 people. Pray for healing for those affected by the Coronavirus.

Care. Care for the practical needs of those affected by the Coronavirus. Help out with babysitting, provide meals, go grocery shopping for the elderly or check on your friends and family.

Share. Share the hope you have in Christ. Post a video of your testimony with #go2020 #hopebeyondfear. Text your testimony or share it over WhatsApp, IG, SnapChat, Tik Tok or Facebook.

GO 2020 starts now!

Pray. Pray for 5 people. Pray for healing for those affected by the Coronavirus.

Care. Care for the practical needs of those affected by the Coronavirus. Help out with babysitting, provide meals, go grocery shopping for the elderly or check on your friends and family.

Share. Share the hope you have in Christ. Post a video of your testimony with #go2020 #hopebeyondfear. Text your testimony or share it over WhatsApp, IG, SnapChat, Tik Tok or Facebook.

CHOLINGA: 

KUSONKHANITSA OKHULUPILIRA 1 MILLION KUTI AKAFIKIRE ANTHU 1 BILLION NDI UTHENGA WABWINO 

MWEZI OCHITIRA UMBONI ndi mbali yapadela ya TSIKU LOCHITIRA UMBONI PA DZIKO LONSE LAPANSI 

MASABATA ASANU AMWEZI WA MEYI 2020 

KODI MUNGATENGE NAWO MBALI MOTANI? 

Pemphelani limodzi ndi mazana mazana a Akhristu mu Sabata yoyambilila ya mwenzi wa Meyi. 

OKHULUPILILA WINA ALIYENSE 

ANTHA KUFIKIRA ANTHU ASANU 

Gawanani Uthenga wa Bwino ndi anzanu, amene akuzungulirani kudela kwanu, ogwira nawo ntchito ndi amubanja mwanu. Chonde satirani malangizo a boma popewa Kolona Vailasi (matenda a COVID 19) potalikirana ndi anzanu. Pempherelani ndi kusamalira osowa. Uzani ena za Uthenga wa bwino kuzera mu masamba a intaneti, mafoni, polemberana kalata monga imelo komanso ngati nzotheka poyankhulana. Umboni wanu utha kusintha mioyo kwa muyaya!

MPINGO ULIWONSE 

UTHA KUKONZA ZOCHITIKA ZOCHITIRA UMBONI 

Potalikirana muthakuuza ena za Uthenga wa Bwino pokwiritsa ntchito makina a intaneti ndi mumagulu ang'ono-ang'ono. Njira imeneyi itha kugwiritsidwanso ntchito pophunzitsa ena za chikhulupiriro, potumiza ma uthenga olimbikitsa ena ndikuthandiza ena. Gwiritsani ntchito njira zilizonse malingana ndi mumene zithu zilili kudela kwanu pofotokozera ena za Uthenga wa Bwino.

ZOCHITIKA 

ZOCHITIKA  

Pemphero  

Pempherani kuti Mulungu alowerere munyengo ino  ya mulili wa Kolona komanso kuti anthu ambiri atembenuke mitima mu mwezi wa Meyi 2020.

 

ZOCHITIKA  

Kufalitsa Uthenga 

Mipingo yokwana 1 million ndi okhulupilila okwana 100 million akhala akuchitira umboni za Uthenga wabwino mu mwezi wa Meyi. 

ZOCHITIKA  

Magulu 

Zonyezani ZIZINDIKIRO ZINAYI pamasamba a intaneti kapena popanga zionetsero zazizindikiro ndi gulu la anthu ena ngati zingatheke.

ZOCHITIKA  

Kusamalira  

Samalirani anthu osowa ndi amene ali mumavuto. Mutha kuonetsera umodzi wanu powathandiza iwo ndizithu  zofunikira pamoyo wawo wa tsiku ndi tsiku.

ZOCHITIKA  

Kuphunzitsa (Kupanga Ophunzira) 

Anthu amene atembenuka mtima aphunzitsidwe ndi kukhazikitsidwa mu mipingo. 

ZOCHITIKA  

Kubatizidwa  

Thawi ya kumapeto kwa Sabata yomaliza ya mwenzi wa Okutobala 2020 mazana a anthu amene atembenuka mtima adzakala akubatizidwa. 

TENGANI MBALI PA MWEZI WOCHITIRA UMBONI MU 2020 

Pezani ka buku ka “Masitepe Atatu” ndi zida zina zompunzitsira.  Lembetsani dzina la mpingo wanu ndi kupereka cholinga chanu. 

GO 2020 ABALE MU UTUMIKI 

Mwezi ochitira umboni uthandizira mpingo wanu kuti ukule ndi chikhalidwe chatsopano chochitira umboni za uthenga wabwino. 

do it your own way!

How to participate

You can participate with your whole denomination, ministry and church through mobilizing and training every believer possible for personal evangelism.. Every church is invited to be involved into planting a new church.

Together we can reach 1 billion with the Gospel! Register today and you will get access to helpful training resources.

JOIN NOW!